Original lyrics
NYTranslation not available yet. Showing the original lyrics.
Chuma chathuchi, tima pereka
Ntima woka kwa tate tipereka
Kuti mpingowo uyende bwinoo
Ntima woka kwa tate tipereka
Ntima woka kwa tate tipereka
Tiye iye tiye
Tikapereke kwa tate
Tiye iye tiye
Tikapereke kwa tate
Ine indilimbe txopereka
Tika woka kwa tate tipereka
Apositoli analibe chuma
Ntima woka kwa tate tipereka
Choyendetsera nacho mpingo
Ntima woka kwa tate tipereka
Ntima woka kwa tate tipereka
Anagulitsa, sinthu zao
Ntima woka kwa tate tipereka
Kuti apeze chuma chao
Ntima woka kwa tate tipereka
Ntima woka kwa tate tipereka
Ndipo anania, ndi safira
Ntima woka kwa tate tipereka
Anagulitsa, mundao wao
Ntima woka kwa tate tipereka
Ntima woka kwa tate tipereka
Koma chumacho, adapereka
Ntima woka kwa tate tipereka
Ndipo china, adabisa
Ntima woka kwa tate tipereka
Petro adati, iwo anania
Ntima woka kwa tate tipereka
Nena zona, pa chuma chanu