Maury
SW

Maury şarkı sözleri

TürWorld Music
Süre4:07
Orijinal dilSW
Görüntülenme3.1K
AaOkuma ayarları
Metin boyutu 18

Orijinal sözler

SW
Translation not available yet. Showing the original lyrics.
Namadingo Kumvetsetsana Inde tinkamvetsetsana Ija inali true love Tinkakondana ah ah ah Zatsogolo lathu Zidali mmanja mwake Mwa Mulungu Koma yemwe adanena Palibe chosatha Sadanane Zonse zimatha ah ah Zimawawa palibe chamuyaya ah ah ah ah Maury adandisiya Maury adakwatiwa Ine zidandiwawa koma (Ululu umatha ah ah ah) Pakapita nthawi ine (Mabala achila ah ah ah) Maury adandisiya komabe (Ululu umatha ah ah ah) Moyo goes on (Mabala achila ah ah ah) Palibe chamuyaya Papita nthawi ine Maury atandisiya Maury adakwatiwa Atapita Maury Nalo dziko lilandikulira Mtima kupweteka nkumangopirira (Kupirira) Pagulu ukumwetulira Kumbali ukusisima Ukulira Maganizo kukumbuka momwe Chikondi chinkakomera Simomwe mtima wako nawonso Umawawira Kutopa ndi kulira maso ku fiila Kufuna kudzimangirira ah ah ah Koma ayi ayi uh huh Zonse zimatha mchimwene wanga Palibe chosatha mchemwali wanga Zimawawa komabe Ululu umatha ah ah ah Papita nthawi komabe Mabala achila ah ah ah Ine Maury adandisiya Komabe ululu umatha ah ah ah Ndipo mabala achila ah ah ah Maury adandisiya Maury adakwatiwa (Palibe chosata ah ah ah) Ndipo palibe chamuya ah ah ah Olo ndalama imatha Iwe kukhala mmaludzi Maudindo amatha Iwe kukhala nobody Olo maludzi amatha Mutaipedza bandulo Inu minyama imatha Iwe kupedza madalitso Ungo limba mtima (Moyo ndi choncho moyo oh oh oh) Tsiku lina udzachira (Moyo ndi choncho moyo oh oh oh)

Namadingo sanatçısından daha fazla

Namadingo →

İlgili şarkı sözleri