Wandibalalisa
Portuguese

Wandibalalisa lyrics

GenrePop
Original languagePortuguese
AaReading settings
Text size 18

Original lyrics

PT
Translation not available yet. Showing the original lyrics.
Mm, yee, no, no, no, koma Zenko B Owo, Nelisa Wandibalalisa Nzeru zanga wamaliza Iwe na ine tikwatulane Owo, Nelisa Wandibalalisa Nzeru zanga wamaliza Iwe na ine tikwatulane, yee, yee 'Ndiwe umandinvetsa kukoma, ine Ndimaona ndikagona, ndiwe Ka thupi kako kokoma, hy, ndisaname Ndimakufila, dona Akanapanda kukulenga, bwenzi ndili single Bwenzi ndikuona akazi opanda ntchito, aah Koma poti ulipo pompano pa dziko, ine Ndikusakasaka mpaka kumene iwe uliko Ndimati ndikakuona, chimwemwe udzaza tsaya Mwayi umenewu ena anautaya Komano ine ndakupeza, ndikugwilitsitse Moti ine ndi wako, wina asakupusitsea (Kolasi) Owo, Nelisa Wandibalalisa Nzeru zanga wamaliza Iwe na ine tikwatulane Owo, Nelisa Wandibalalisa Nzeru zanga wamaliza Iwe na ine tikwatulane, yee, yee Ndikuthokoza Mulungu pondipasa ka ngenge Moti chaka chino, basi ndikatenge Ndikaulemu, komanso kopanda phuma Abale, ndisaname, ine ndapeza ka tsuna Pa two tayesela kuchotsa one Undiuze kodi aswer upeza chani? Kukongola kwako, mndani angachite makani? Ndimakuuza kuti ndiwe number one (Kolasi) Owo, Nelisa Wandibalalisa Nzeru zanga wamaliza Iwe na ine tikwatulane Owo, Nelisa Wandibalalisa Nzeru zanga wamaliza Iwe na ine tikwatulane, yee, yee Zenko B Production Records Ayi

Related lyrics